Letras
[intro]
mmmm ndine Alex bitoni.
kaya mulibwa?
[chorus]
mulibwanji maheta.
mulibwanji oheta.
mulibwanji oDisa ine.
mulibwanji mahuule.
ine ndingopeleka moni,ndati moni.
moni,moni,moni.
Inu ndati moni,moni,moni.
[vers1]
Pali ena aja!
amandidisa aja.
Pali ajawa amatiseka kutinena kuti sitizahita eya kumadisa.
kumajeda kumatumbwa.
achite manyazi ndisateye nthawi ndingoti.
[chorus]
mulibwanji maheta.
mulibwanji oheta.
mulibwanji oDisa ine.
mulibwanji mahuule.
ine ndingopeleka moni,ndati moni.
moni,moni,moni.
Inu ndati moni,moni,moni.
[vers2]
nonse mudziwe kuti ndilipano chifukwa cha yehova.
mukukambilana zonditsitsa mukunama.
ine ndili nji,nji,nji.
ine ndili nji,Kwa yehova .
muchite manyazi.
ondifunila zoyipa.
eya ndati Kwa nonse.
ndisateye nthawi ndingoti.
[chorus]
mulibwanji maheta.
mulibwanji oheta.
mulibwanji oDisa ine.
mulibwanji mahuule.
ine ndingopeleka moni,ndati moni.
moni,moni,moni.
Inu ndati moni,moni,moni.
ALEX BITON ON THE BEARTS.
mmmm ndine Alex bitoni.
kaya mulibwa?
[chorus]
mulibwanji maheta.
mulibwanji oheta.
mulibwanji oDisa ine.
mulibwanji mahuule.
ine ndingopeleka moni,ndati moni.
moni,moni,moni.
Inu ndati moni,moni,moni.
[vers1]
Pali ena aja!
amandidisa aja.
Pali ajawa amatiseka kutinena kuti sitizahita eya kumadisa.
kumajeda kumatumbwa.
achite manyazi ndisateye nthawi ndingoti.
[chorus]
mulibwanji maheta.
mulibwanji oheta.
mulibwanji oDisa ine.
mulibwanji mahuule.
ine ndingopeleka moni,ndati moni.
moni,moni,moni.
Inu ndati moni,moni,moni.
[vers2]
nonse mudziwe kuti ndilipano chifukwa cha yehova.
mukukambilana zonditsitsa mukunama.
ine ndili nji,nji,nji.
ine ndili nji,Kwa yehova .
muchite manyazi.
ondifunila zoyipa.
eya ndati Kwa nonse.
ndisateye nthawi ndingoti.
[chorus]
mulibwanji maheta.
mulibwanji oheta.
mulibwanji oDisa ine.
mulibwanji mahuule.
ine ndingopeleka moni,ndati moni.
moni,moni,moni.
Inu ndati moni,moni,moni.
ALEX BITON ON THE BEARTS.