makolo cover art

Creat pe mar. 22, 2026

Versuri

Intro
Mmmm ndine ALEX BITON
[Vers1]
Mwadzuka bwanji kutauniko?
Kukakhala kuno sikuli boo
Munangopita kutauniko inu kimudzi kuno mwayiwalako
banbo kutauniko mukubeba ife matumba tikusenza nyama yang'ombe mukudyela ife masamba tikudyelaaa ndati mubwele ee inu mubwele ee inu Ababa ine sinzayiwala zomwe mwapanga kubanja lanuli kulingongole muzabwenzeee inu Ababa muzabwenze.

[Corus]
Bwelelani oooo bwelelani eeee bwelelani kumudzi kuno bwelelani inu kuthawa kumudzi kupita kutauni bwelelani Ife kunoko kumudzi tikukhala mmaluzi bwelelani oooo.

[Vers2]
Mukuti tukhala chonchi Kodi kumangodikila kumunda tayambila kulima inu osatulukila ndiye anzanu analipo mmene munkachoka kuno chimanga chanu chathanso tagona choncho dzulo oooo ndalama zanu zathanso nyumaba yanuyi yathanso sukulu Ana asiyanso akuti fizi yakwelanso oo ndalama zanu zathanso nyumaba yanuyi yathanso sukulu Ana asiyanso akuti fizi yakwelanso oo

[Corus]
Bwelelani oooo bwelelani eeee bwelelani kumudzi kuno bwelelani inu kuthawa kumudzi kupita kutauni bwelelani Ife kunoko kumudzi tikukhala mmaluzi bwelelani oooo.Bwelelani oooo bwelelani eeee bwelelani kumudzi kuno bwelelani inu kuthawa kumudzi kupita kutauni bwelelani Ife kunoko kumudzi tikukhala mmaluzi bwelelani oooo.

ALEX BITON ON THE BEATS.