mavuto cover art

Creat pe mai 31, 2026

Versuri

(intro)
Mmmm ndine Alex biton.

(Vers1)
Chikondi, chikondi.
Chikondi gayezi pena ndichovuta.
Zachikondi sizi mafunika kufuntha.
Ndaziwona zachikondi sizi nali kumbali yanga.
Koma ine ndichani chinandigwela Kaya.
Ndinayesela kukonda gayez akaziwa ndi oipa.
Anandisakaza ndikundisiya mumdima.
Zachikondi ndazisiya sindikamba zambili.
ingodikilani vesi two.

(Corus)
Zachikondi ndazisiya.
Zachikondi kwaine osakambanso.
Mumati chikondi ndi chisangalalo.
Nanga ndaziona inezi ndizichani.
Ndawona mavuto,ine ndawona mazunzo.
Ndawona zambili ndawona magobo.

(Vers2)
Abale anga mundimvele chonde.
Ndinali ndi chibwenzi chimakhala kwa Sande.
Osanama gayezi nkaziyu ndimkamukonda.
Koma zoipa ineyo mtangodwala.
Free weeks no text no kundikhola.
After kuchila inali sande.
Ndinangodabwa call kwa nkaz wakwa sande.
Amvekele (hello Bea kd mulipo?).ine shaa muntima munadzazana ndi mkwiyo.
Poganizila zomwe anandichita.
Free weeks ndikudwala.
Koma iye osalabada.
Wawona ndachila pano akundikhola.
Akufuna moyo wanga.
kapena akufuna chuma changa.
Gayezi zachikondizi ndazisiya.

(Corus)
Zachikondi ndazisiya.
Zachikondi kwaine osakambanso.
Mumati chikondi ndi chisangalalo.
Nanga ndaziona inezi ndizichani.
Ndawona mavuto,ine ndawona mazunzo.
Ndawona zambili ndawona magobo.
Zachikondi ndazisiya.
Zachikondi kwaine osakambanso.
Mumati chikondi ndi chisangalalo.
Nanga ndaziona inezi ndizichani.
Ndawona mavuto,ine ndawona mazunzo.
Ndawona zambili ndawona magobo.
ALEX BITON ON THE BEATS