nkhuku cover art

Creat pe apr. 17, 2026

Versuri

Intro
Ndine Alex biton.
Ooo bitoni.6 mponee,ineyo aGeni.
Palina ee,palina ee,palina ee.
Palina ee,palina ee,palina ee.
[Vers1]
Hello akayidi takulandilani.
Kuti mubwele kuno chachitika ndichani.
Monga nyapala wankulu,akayidi akulu.
Ndineyo ndikuyang'anila.
Muzinena zonse munalakwa.
Anthu oyipa timalakwa.
Munena anthu onse munawapha.
Kupha anzanu osalakwa.
Tiyambile kukonako!
Apeze malo ogona konko.
iwe zuka pamenepo!.
Usazaginenso mmaso mwako.
Zimene tinapanga tiulule.
Nkhani ya banja tiulule.
Ngati unapha nzako ing'alule .Alex biton adziwee.
[Corus]
Nanga iwe unaba chani?
Ndikaba injini ya benzi kubangwee.
Nanga inu Mani?.
Ndinakaba 4 mita ine kwa mmwenye.
iwe unaba chani?
Ndinakatenga ayifoni 6 kwanebako!
Nanga inu Mani?
Ndinamenya mkazi mpaka kukomoka.
Bola inu,ife inali nkhuku ase,nkhuku ase,nkhuku ase.
Mpaka zaka folo,kundende.
Chifukwa Cha nkhuku ase.
Eti nkhuku ase,nkhuku ase nkhuku ase.
Mpaka kulawa unyolo, kundende.
Chifukwa Cha nkhuku ase.
[Vers2]
inu!,Chete!,Chete.
mukupanga phokoso mukhale chete.
Kodi apa odi.
Mukupanga phokoso mukhale chete.
Kuzimva a! Zondisekelela ayi.iwe.
Nkhuku nchani ife tinaswa mazila awili.
Nde amazitchula unyambala ndani pano?[uyuyu].
i! iweyotu undisamale kuno.
ine ching'ombe ukati kukula chimutu.
Kundiphyesa ntima magayezi inu,ine ayi.
Kuno ndi ku pilizoni simuli kwanu. mukhale ndi disipilini.
Ndikupita komwe mnali ndisamve phokoso.
Maka ichi kuzimva umbadwa.
Ndiye paliibe zokambilananso.
izizi ndanene mufune musafuune.

[Corus]
Nanga iwe unaba chani?
Ndikaba injini ya benzi kubangwee.
Nanga inu Mani?.
Ndinakaba 4 mita ine kwa mmwenye.
iwe unaba chani?
Ndinakatenga ayifoni 6 kwanebako!
Nanga inu Mani?
Ndinamenya mkazi mpaka kukomoka.
Bola inu,ife inali nkhuku ase,nkhuku ase,nkhuku ase.
Mpaka zaka folo,kundende.
Chifukwa Cha nkhuku ase.
Eti nkhuku ase,nkhuku ase nkhuku ase.
Mpaka kulawa unyolo, kundende.
Chifukwa Cha nkhuku ase.

ALEX BITON ON THE BEATS.