mutitsogolele yehova cover art

mutitsogolele yehova

A
ALEX BITON

Creat pe mar. 23, 2026

Versuri

intro
mmmm ndine Alex bitoni

corus
ambuye mutidalitse mutipase nzelu mutipasenso mphamvu mutiyang'anile mutisamalile ndinu nokha amene mungatitetezele ndikupempha mutitsogolele

vers

ndinu mbambande yehova
mumatidalitsa nthawi zonse pamavuto pantendele mulinafe opanda inu ndife ndani?opanda inu tilichabe mutitsogolele nthawi zonse tisatayikee
eya ndife ochimwa tikuvomeleza koma tikudziwa kulapa kwathu mukuvomeza simungatitaye ndipo simungatinyoze.

corus
ambuye datidalitse mutipase nzelu mutipasenso mphamvu mutiyang'anile mutisamalile ndinu nokha amene mungatitetezele ndikupempha mutitsogolele

vers2
ndinu nthunzi wamoyo!!tisaname payinuyo tisamila tikudziwa simungalole kuti munyanja yayinfa tizimila ndinu zonse zaifeyoo simu sitizazima ngati mooto! mumakhala nafe pamavuto pantendele monga Ife Ana Anu simungalole tizunzike ineyo Alex bitoni ndagwada pamaondo Anu pemphelo langali mulimvele.

corus
ambuye datidalitse mutipase nzelu mutipasenso mphamvu mutiyang'anile mutisamalile ndinu nokha amene mungatitetezele ndikupempha mutitsogolele

vers

ndinu mbambande yehova
mumatidalitsa nthawi zonse pamavuto pantendele mulinafe opanda inu ndife ndani?opanda inu tilichabe mutitsogolele nthawi zonse tisatayikee

corus
ambuye mutidalitse mutipase nzelu mutipasenso mphamvu mutiyang'anile mutisamalile ndinu nokha amene mungatitetezele ndikupempha mutitsogolele.ambuye mutidalitse mutipase nzelu mutipasenso mphamvu mutiyang'anile mutisamalile ndinu nokha amene mungatitetezele ndikupempha mutitsogolele

ALEX BITON ON THE BEATS.