Letra
[intro]
Mmmmm a FB kamakani!!.Mr makani music.
[Vers1]
Anti nanga bwanji mukukhesa mimsozi.
Mmene kwachela mmamawa.
Simukusangalala kudali chonchi.
Pali awili Pali anthu ndine mchimwene wako.
Ndimasukile mzelu mkupangwa.
Mwina ukundikayikila koma ndine m'balewako.
Koma ngati zili zamamuna uja.
Pempho langa ndiloti?
[Corus]
Mukapilile, mukapilile anti.
Chikondi ndichovuta mukapilile anti.
Nthawi Zina kusangalala.
Nthawi Zina ndikumalila.
Ukachitengela kwambili chikondi.
Utha kusintha amuna.
Ndikupempha mukapilile, mukapilile anti.
[Vers2]
Ndiwamasiye mnkaziyi.
Chonde kamusamaleni.
Zikavuta zimatha ndikukambilana.
Chimenecho ndichisinsi Cha banja.
Sakufuna kusintha amuna.
Masiketi ndi ambili.
mkazi ndi uyu omwe mwafuna.
Muzipanga zoti.
Kunyumba kwanu ndizibwela.
Ungapangise ndiwe mmamuna.
Nawenso joyi pempho lanaga ndiloti?
[Corus]
Mukapilile, mukapilile anti.
Chikondi ndichovuta mukapilile anti.
Nthawi Zina kusangalala.
Nthawi Zina ndikumalila.
Ukachitengela kwambili chikondi.
Utha kusintha amuna.
Ndikupempha mukapilile, mukapilile anti.
Mukapilile, mukapilile anti.
Chikondi ndichovuta mukapilile anti.
Nthawi Zina kusangalala.
Nthawi Zina ndikumalila.
Ukachitengela kwambili chikondi.
Utha kusintha amuna.
Ndikupempha mukapilile, mukapilile anti.
ALEX BITON ON THE BEATS.
Mmmmm a FB kamakani!!.Mr makani music.
[Vers1]
Anti nanga bwanji mukukhesa mimsozi.
Mmene kwachela mmamawa.
Simukusangalala kudali chonchi.
Pali awili Pali anthu ndine mchimwene wako.
Ndimasukile mzelu mkupangwa.
Mwina ukundikayikila koma ndine m'balewako.
Koma ngati zili zamamuna uja.
Pempho langa ndiloti?
[Corus]
Mukapilile, mukapilile anti.
Chikondi ndichovuta mukapilile anti.
Nthawi Zina kusangalala.
Nthawi Zina ndikumalila.
Ukachitengela kwambili chikondi.
Utha kusintha amuna.
Ndikupempha mukapilile, mukapilile anti.
[Vers2]
Ndiwamasiye mnkaziyi.
Chonde kamusamaleni.
Zikavuta zimatha ndikukambilana.
Chimenecho ndichisinsi Cha banja.
Sakufuna kusintha amuna.
Masiketi ndi ambili.
mkazi ndi uyu omwe mwafuna.
Muzipanga zoti.
Kunyumba kwanu ndizibwela.
Ungapangise ndiwe mmamuna.
Nawenso joyi pempho lanaga ndiloti?
[Corus]
Mukapilile, mukapilile anti.
Chikondi ndichovuta mukapilile anti.
Nthawi Zina kusangalala.
Nthawi Zina ndikumalila.
Ukachitengela kwambili chikondi.
Utha kusintha amuna.
Ndikupempha mukapilile, mukapilile anti.
Mukapilile, mukapilile anti.
Chikondi ndichovuta mukapilile anti.
Nthawi Zina kusangalala.
Nthawi Zina ndikumalila.
Ukachitengela kwambili chikondi.
Utha kusintha amuna.
Ndikupempha mukapilile, mukapilile anti.
ALEX BITON ON THE BEATS.