Letra
(intro)
Fulesho keyi.
(Vers1)
Abale anga chonde ndithandizeni.
Tsogolo Yanga ipitilizeni sindinkadziwa.
Chomwe ndikuchita lelo tawonani.
Ndikudowa chochita ndikungokhalila.
Moyo ovutika pa banja panga ine kushupika.
Ndinakwatila Pano ndikuvutika.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Kusukulu mkumandikankhisila.
Sindinkafuna ndinasankha banjayi.
Ndikusanzika pano umphawi unandiyanja.
(Corus)
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
(Vers2)
Oo sindingachitile mwina.
Pakuti zinthuzi ndizomwe ndinkafuna.
Ndikudowa Tate ndisamalileni ana angawa.
Achengeteleni zikomo Tate.
Pamoyo Uno sindinkadziwa kuti ndizabweza chani.
Zofoka zanga zamoyo Uno.
Chonde muponye kunja.
Pena mayi anga ankandilangiza.
koma ndimkawona ngati akundinamiza.
Mwina mwake ndingochoka dziko muno.
Umphawi wanga unandiyanja.
(Corus)
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
ALEX BITON ON THE BEATS
Fulesho keyi.
(Vers1)
Abale anga chonde ndithandizeni.
Tsogolo Yanga ipitilizeni sindinkadziwa.
Chomwe ndikuchita lelo tawonani.
Ndikudowa chochita ndikungokhalila.
Moyo ovutika pa banja panga ine kushupika.
Ndinakwatila Pano ndikuvutika.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Kusukulu mkumandikankhisila.
Sindinkafuna ndinasankha banjayi.
Ndikusanzika pano umphawi unandiyanja.
(Corus)
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
(Vers2)
Oo sindingachitile mwina.
Pakuti zinthuzi ndizomwe ndinkafuna.
Ndikudowa Tate ndisamalileni ana angawa.
Achengeteleni zikomo Tate.
Pamoyo Uno sindinkadziwa kuti ndizabweza chani.
Zofoka zanga zamoyo Uno.
Chonde muponye kunja.
Pena mayi anga ankandilangiza.
koma ndimkawona ngati akundinamiza.
Mwina mwake ndingochoka dziko muno.
Umphawi wanga unandiyanja.
(Corus)
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
Ndinasiya geli kufuna banjayi.
Abale wanga chonde ndithandizeni.
Ndinasiya geli kufuna banja.
Sindinkadziwa chomwe ndikuchita.
ALEX BITON ON THE BEATS