munakumana kuti? cover art

munakumana kuti?

A
Alexander Biton

Creada el mar. 24, 2026

Letra

[intro]
Mmmmmm ndine Alex bitoni.
Munakumana kuti?inu munakumana kuti?
[Corus]
mumamvetsana kukoma.
Mumamvetsana kuwawa.kodi munakumana kutiko? inu munakumana kuti.munakumana kutiko?

[Vers1]
Achimwene mulinchikondi awuzeni anthu kuti munakumana bwanji.muyime pachuulu muwauze anthu kuti ndinkazi wanuyoo eya ndimamuna wanuyoo munakumana kuti?poti chikondi chinkakuvutani,banja inkakusowani.munakumana kutiko?

[Corus]
mumamvetsana kukoma.
Mumamvetsana kuwawa.kodi munakumana kutiko? inu munakumana kuti.munakumana kutiko?

[Vers2]
Achemwali mulinchikondi pachiyambi zinkakuvutani.muwauze anthu kuti wachikondi wanuyoo munamupeza kuti? munakumana kuti, munakumana kutiko? chikondi kwayinu chinali chovuta kozi munali ofuntha koma munasintha, chikondi mwachipeza mwayenela kuthokoza eya koma munakumana kutiko?

[Corus]
mumamvetsana kukoma.
Mumamvetsana kuwawa.kodi munakumana kutiko? inu munakumana kuti.munakumana kutiko?

[Vers3]
chikondi ndichovuta kumvetsa life imabowa kukhala opanda nkazi,imabowa kukhala opanda wachikondi,anthu amakumana mnjila zosiyana siyana,ena munakumana kubala,ena munakumana kuchamba,ena munakumana kutchetchi inu mkupasana ma minzi,enawa anakumana kuchipatalako chifukwa choti anadwala.ndinjila zambili zopezela wachikondi nanga wanuyoo munamupeza kuti?inu munakumana kutikoooo?


[Corus]
mumamvetsana kukoma.
Mumamvetsana kuwawa.kodi munakumana kutiko? inu munakumana kuti.munakumana kutiko? Mmm mmm

ALEX BITON ON THE BEATS.

inu munakumana kuti?