ndikulila cover art

ndikulila

L
Lamusa Haji

Created Apr 12, 2026

Lyrics

[intro]
mmmm a fb kamakani.
Mr makani music

[vers1]
oo ndikamakhala ndekha ndimazifunsa.
uu kulingalila nyengo zanga mene ziyendela.
we sukulu ndinasiyila panjila we.
koma anzanga ndinabadwa pa umphawi.
kukulilanso pa umasiye.
nditabadwa Makolo anga sanachedwe kundisiya.
oo anayamba ndi mayi anatsala ndi Bambo.
bambo nditatsala nawo.
anakwatila nkazi oti andisamalile.
komabe zilichoncho nawonso bambo anandisiya.
ndipamene ndinayamba kulila.

[corus]
koma mayiii,amayi.
mukundisiyilanji.
koma adadii, adadii.
ine ndinalakwanji.
kuchoka sachoka choncho koma.
kundipasa dzina LA umasiye inu amayi.
ndekha ndekha mudziko LA umphawiyii.

[vers2]
ndiye tamvelani amzanga.
nawonso amayi aja anakwatidwa kwina.
zinasala ndi nkhawa ndekhala kumangolila.
ndinayamba moyo obalalika osowa chochita.
nditatelo ndinayamba kujiya.
komabe sizimathaa.
ndipamene ndinaziwa umasiye ndi owawa.
komabe moyo wanga mene uyendela.ndichite bwanji mwana wanu ine fb kamakani.ndikamakhala pansi ndikumangolila.

[corus]
koma mayiii,amayi.
mukundisiyilanji.
koma adadii, adadii.
ine ndinalakwanji.
kuchoka sachoka choncho koma.
kundipasa dzina LA umasiye inu amayi.
ndekha ndekha mudziko LA umphawiyii.
koma mayiii,amayi.
mukundisiyilanji.
koma adadii, adadii.
ine ndinalakwanji.
kuchoka sachoka choncho koma.
kundipasa dzina LA umasiye inu amayi.
ndekha ndekha mudziko LA umphawiyii.

ALEX BITON ON THE BEATS.