ndak cover art

Created May 17, 2026

Lyrics

yeyeyee man samzy

iwe ukawauze kuti ndakukonda iwe chomwe ndikufuna usakabise

anthu akumudi kwathu iwe akakuone pa kukomgola kwako Kwandisintha ine azibale anga iwe akuone achina Sige achina tamala akakuone iwe

iwe ukawauze kuti ndakukonda iwe chomwe ndikufuna usakabise

ine ndikuona kuchedwa ndikufuna iwe ndikutengele kwathu ine ndikufuna iwe wekha basi azidzanga akufuna akakutchule alamu ndipo abale anga akufuna kutchula ayini achina evidesi akufuna kukamba za iwe achina patirisha onse akuwone iwe

iwe ukawauze kuti ndakukonda iwe chonde ndikufuna usakabise ndaimba ndine man samzy kuchokela ku

victor osman on the bit