Duwa cover art

Создано май 24, 2026

Тексты

[Intro]

Dabiyu Steveeeee........!

[Verse 1]

Ndikaponya maso ndimaona iwe.
Ndikatseka maso ndimaona iwe.
Kukongola kochititsa kaso.........
Ndilore khale oyamba kupeleka mphatso....

Ndiwe duwa lowala pakati pa dimba.
Ndiwe nyali yosazima.
Mu dima mathwanima...
Nyenyez yanga yowala kunthambo.....

Hook

Ukanditalikira, ndimakusowa.
Ukapanda kuimba phone ndimadwala.
Ndikakhala ndiwe, chimwemwe nsaya.
Duwa la.....nga!!!!!!!!!.

[CHORUS]

Ndiwe duwa......
Lowala nkat mwa mtima mwanga ndiweeeeeee.
Sumazima.
Ndimakukonda.

Every...........whereeyyyy.
You go.!!!!!!!
Always you be my mind.
Duwa langaaaaa. mmmmmh eeeeeh yaaaah!!!!!!.


[VERSE 2]

Umakhala kutali ndine baby.
Koma mtima wanga umakhala nawe.
More times, every day.
I know you miss me and i miss you too.
But makhala chifupi ndiwe.

Likatha tsiku osacheza texting.
My life i fe........el pain.
Kumaganiza ukuta, ukupanga chan.
Komabe sindikaika uli nane duwa langa.

[Hook ]

Ukanditalikira, ndimakusowa.
Ukapanda kuimba phone ndimadwala.
Ndikakhala ndiwe, chimwemwe nsaya.
Duwa la.....nga!!!!!!!!!.

[CHORUS]

Ndiwe duwa......
(Ooooooooooh!!!)
Lowala nkat mwa mtima mwanga ndiweeeeeee.
(Mmmmmmmmmmh)
Sumazima.
Ndimakukonda.

Every...........whereeyyyy.
You go.!!!!!!!
Always you be my mind.
Duwa langaaaaa. mmmmmh eeeeeh yaaaah!!!!!!.

[Pre Hook]

Ukanditalikira, ndimakusowa.
Ukapanda kuimba phone ndimadwala.
Ndikakhala ndiwe, chimwemwe nsaya.
Duwa la.....nga!!!!!!!!!.

[CHORUS]

Ndiwe duwa......
(Baby eeeeeh iiiii)
Lowala nkat mwa mtima mwanga ndiweeeeeee.
Sumazima.
(Mmmmmh nananah)
Ndimakukonda.

Every...........whereeyyyy.
You go.!!!!!!!
Always you be my mind.
Duwa langaaaaa. mmmmmh eeeeeh yaaaah!!!!!!.

[Upbeat]