dark ft ikenga cover art

Создано апр 18, 2026

Тексты

intro

Dark. venom. venom. ifendamalawiiii. intro gaye!!!!

chorus

tsiku lina ndidzamwalila anthu ena adzandilila lekelenji kusangalala pamene ine ndili moyo
tsikuli ndidzamwalila anthu ena adzandifochela lekelenji kusangalala pamene ine ndilimoyo
ndikapeza ndalama ndimweko fanta ndikapeza ndalama ndidyeko soseji pamene ine ndili moyo.

verse

ndimweko malawi jini. kuchekuche konyagi wavutayiii ndalama zikatha ndilolela eee kupinyolitsa tayiii ndagulitsa fodya nandolo soya mtedza ndine bambo apemphelo kwathu mkumayaniii. kudedza. lekelenji kusangalala pamene ine ndilimoyooooo

chorus

tsiku lina ndidzamwalila anthu ena adzandilila lekelenji kusangalala pamene ine ndili moyo
tsikuli ndidzamwalila anthu ena adzandifochela lekelenji kusangalala pamene ine ndilimoyo
ndikapeza ndalama ndimweko fanta ndikapeza ndalama ndidyeko soseji pamene ine ndili moyo.

verse2

ikenga the pango. wachiyawo wangalusa. ndilekelenji. kumwako mowa. chosecho moyowu. ndiwaufupi. tandilekeni ndinjoyeletu. poti. kumanda. kulibe. matsuna. gwileko ka jeni. tionge. ndi. magi. mwina. moyowu. mkuwupepesa nde ndilekelenji kusangalala. pamene ine. ndilimoyooo

chorus

tsiku lina ndidzamwalila anthu ena adzandilila lekelenji kusangalala pamene ine ndili moyo
tsikuli ndidzamwalila anthu ena adzandifochela lekelenji kusangalala pamene ine ndilimoyo
ndikapeza ndalama ndimweko fanta ndikapeza ndalama ndidyeko soseji pamene ine ndili moyo