nkhan yanga pati 1 cover art

nkhan yanga pati 1

B
Biton Alex

Создано мар 24, 2026

Тексты

[intro]
Mmmmn ndine Alex biton.
E ase BEN10 ndadusa munyengo zowawa ndisaname ndye khala pompo umveko nkhani yanga.

[Vers]
Abambo anga anakwatila nkazi.
Anakhala nthawi yayitali kusowa mphatso yamwana kwanthawi yayitali. koma bambo sanasiye kupemphelaa mpaka akazi awo pakati anamapenga.banja inayamba kusangalala kuti mulunga awadalitsa ndi mphatso yamwana ndipo akhala ndi mwana koma chikudza sichiyimba ng'oma zomvesa chisoni nthawi yokachila imfa inabwela pakati pawo ndikutenga mwana obadwayo mbanja linalila yiiiiiii!!!!!!!! Mayoooooo!!!!!!!!.kupita kukamuyika mwana osalakwa nyimbo yachisoni ikumveka.aaachimweeee,achimwee,achimwee ee achimwe, achimwe ee achimwe.satana sinasiyile pompo anabwelesanso nthenda m'banjamo zinapezeka kuti mayiwo sazabelekanso mpaka kale zachisoni eeee ase ben10 ingodila pati thu kozi ndayambapo kulila.
ikani pati thu!!!.
ALEX BITON ON THE BEATS.