Letra
Nabola kale lija
Nabola ndikukhala Ndekha muja!!
Ndinkakhala mosangalala
Koma ndimene ndinalowa Banjamu
Ndinaziputila Mavuto!!
Oh ine!!!
Amayo oh ine!!
Nyumba kumalipila Ndekha
Anah Fizi kumalipila Ndekha
Chakudya kumagula Ndekha
Ndalama mumazipeza
Koma komwe zimapita
sikumadziwika!!
(chorus)
Anthu akamati zikundiyendela
Ndimangoti zowonadi zikuyenda
Chosecho pasi pamtima ndikuva kuwawa
Ena amati Banja landiyanja
Mamuna akundisamala
Osadziwa kuti ndine ndikumusamala
Anandipeza ndili ndi Anah awili
Analonjeza kuti azawasamala
Koma lelo ndikudabwa kuti Kodi
Ndapezaso Mwana wina wa Chitatu
Chifukwatu chili chose Ndinapanga Ndekha pa Nkhomo
Anah sanawagulileko Olo chovala
Ndiye mwina Amwali mukudabwa
Kuti bwanji sindikubwelela wina Mwana
Ine ndimazifuda kuti ngati akukanika kuveka olo kudyetsa Anawa
Ndiye azandipatse Mwana wake eeeh
Ine ndizavutika ndizavutika ndisaname
(verse)
Azanga Azanga!
Ndithandizeni!!
Ndinalifuna Banja ine oh
Ndithandizeni!!
Ndipange naye bwanji Mamunayi!!
Abale ndithandizeni
Kapena mwina ndipilile ine!!
Oh Abale ndithandizeni!!
Nabola paja poyamba paja
Zinali bwino(ndikukhala Ndekha)
Amayi kuno ndikulila muntima
Misozi yosatha
Chikondi chake Mamunayi ndichabodza
Anabwela ndi nkhope ya Chikondi
Osadziwa kuti ndi nkhalamo
Ichi ndi chindele
Amayi uyu ndi Ntchewe
Ndili pamoto ine
Amayi uyu ndi Chibwatiko Cha Mamuna
(chorus)
Banja lanji ili Bambo
Lokhalila kukudandawulani
Nkhalidwe lanu loyipa
Munayamba kuliwonetsa ndi kale
Ndinkati mwina muzasitha
Koma apa, aah zanyanya!!
Ndili pa Banja koma
Ndine Batchala!!
Chimamuna ichi ndi Chi Mfiti!!
Ndalama zanga akufuna kundiwonongela!!
Ndikafusa amakalipa penaso kundimenya!!
Amanditenga ngati ine Ng'ombe yake
Yongomulimila ndalama iye ndikumakolala!!
Nabola ndikukhala Ndekha muja!!
Ndinkakhala mosangalala
Koma ndimene ndinalowa Banjamu
Ndinaziputila Mavuto!!
Oh ine!!!
Amayo oh ine!!
Nyumba kumalipila Ndekha
Anah Fizi kumalipila Ndekha
Chakudya kumagula Ndekha
Ndalama mumazipeza
Koma komwe zimapita
sikumadziwika!!
(chorus)
Anthu akamati zikundiyendela
Ndimangoti zowonadi zikuyenda
Chosecho pasi pamtima ndikuva kuwawa
Ena amati Banja landiyanja
Mamuna akundisamala
Osadziwa kuti ndine ndikumusamala
Anandipeza ndili ndi Anah awili
Analonjeza kuti azawasamala
Koma lelo ndikudabwa kuti Kodi
Ndapezaso Mwana wina wa Chitatu
Chifukwatu chili chose Ndinapanga Ndekha pa Nkhomo
Anah sanawagulileko Olo chovala
Ndiye mwina Amwali mukudabwa
Kuti bwanji sindikubwelela wina Mwana
Ine ndimazifuda kuti ngati akukanika kuveka olo kudyetsa Anawa
Ndiye azandipatse Mwana wake eeeh
Ine ndizavutika ndizavutika ndisaname
(verse)
Azanga Azanga!
Ndithandizeni!!
Ndinalifuna Banja ine oh
Ndithandizeni!!
Ndipange naye bwanji Mamunayi!!
Abale ndithandizeni
Kapena mwina ndipilile ine!!
Oh Abale ndithandizeni!!
Nabola paja poyamba paja
Zinali bwino(ndikukhala Ndekha)
Amayi kuno ndikulila muntima
Misozi yosatha
Chikondi chake Mamunayi ndichabodza
Anabwela ndi nkhope ya Chikondi
Osadziwa kuti ndi nkhalamo
Ichi ndi chindele
Amayi uyu ndi Ntchewe
Ndili pamoto ine
Amayi uyu ndi Chibwatiko Cha Mamuna
(chorus)
Banja lanji ili Bambo
Lokhalila kukudandawulani
Nkhalidwe lanu loyipa
Munayamba kuliwonetsa ndi kale
Ndinkati mwina muzasitha
Koma apa, aah zanyanya!!
Ndili pa Banja koma
Ndine Batchala!!
Chimamuna ichi ndi Chi Mfiti!!
Ndalama zanga akufuna kundiwonongela!!
Ndikafusa amakalipa penaso kundimenya!!
Amanditenga ngati ine Ng'ombe yake
Yongomulimila ndalama iye ndikumakolala!!