makolo cover art

Créé le mai 31, 2026

Paroles

(intro)
Me name chifundo from chitimbe.

(Vers1)
Sindizalola wina azakunyozeni.
Sindizalola wina azakulozeni Chala.
Chikondi chimene mumawonesa payineyo.
Ndingabwenze chani nanga.
Kundisamalila ndili wang'ono.
Ndkadwala kuchipatala mumandipititsa.
Ndikalakwisa inuyo mumandilangiza.
Ndipamene payinu ndimayamika.

(Corus)
Ndimakunyadilaniii.
Ndimakunyadilani amama.
Ooo pondisamalila kufikana Lelo.
Ndimakunyadilani amama.
Ndikaphula seen misonzi mumakhesa.
Ndipempha wakumwambayo akuyang'anileni Inu adadi.

(Vers2)
Ngati unyoza makolo mzanga iwe imva.
Pali amzako akusowa makolo.
Ukakhala ndi makolo ndiwe mfulu.
Dziwa makolo ndi chishango.
Amakutetezela pachili chonse.
ine ndi chifundo mkona ndayima pano.
Ndikuyamika amayi anga andisamalila.
Abambo anga andichengetela.
Ndipamene ndimayamika.

(Corus)
Ndimakunyadilaniii.
Ndimakunyadilani amama.
Ooo pondisamalila kufikana Lelo.
Ndimakunyadilani amama.
Ndikaphula seen misonzi mumakhesa.
Ndipempha wakumwambayo akuyang'anileni Inu adadi.
Ndimakunyadilaniii.
Ndimakunyadilani amama.
Ooo pondisamalila kufikana Lelo.
Ndimakunyadilani amama.
Ndikaphula seen misonzi mumakhesa.
Ndipempha wakumwambayo akuyang'anileni Inu adadi.
ALEX BITON ON THE BEATS