Paroles
(intro)
Aefubi kamakani.mr makani music.
(Corus)
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
(Vers1)
Ndili ndi mkazi wina izi ukuziwa.
Koma iwe sulabada umandikondabe.
Nanenso ndimalimba ntima.
Ndipamene ndimakukondabe.
Koma akwanu safuna.
Ati upeze wina mamuna.
Amati ineyo sindikukuyenela.
Ndine bubuda ndilibe kanthu.
Koma timakondana iwe ndi inee.
(Corus)
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
(Vers2)
Kundikonda ine sikuti ndiwe opusa.
Komabe sumafuna kusintha amuna.
Chiganizo chabwino ngati ichi.
Usazachichose mmaganizo mwako.
Umadziwa zoti kunjaku kulimatenda.
Ndipati sufuna kukonda wina.
Olo akwanu amati zayine uyiwale.
Ndipamene umandikondabe.
Nanenso ndidzakukonda.
Koma vuto ndiakwanu aja.
Ndizoti sandifuna.
Sindikudziwa kuti ndidzatani.
Ndiwe amene ungandilimbitse mtimaa.
(Corus)
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
ALEX BITON ON THE BEATS
Aefubi kamakani.mr makani music.
(Corus)
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
(Vers1)
Ndili ndi mkazi wina izi ukuziwa.
Koma iwe sulabada umandikondabe.
Nanenso ndimalimba ntima.
Ndipamene ndimakukondabe.
Koma akwanu safuna.
Ati upeze wina mamuna.
Amati ineyo sindikukuyenela.
Ndine bubuda ndilibe kanthu.
Koma timakondana iwe ndi inee.
(Corus)
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
(Vers2)
Kundikonda ine sikuti ndiwe opusa.
Komabe sumafuna kusintha amuna.
Chiganizo chabwino ngati ichi.
Usazachichose mmaganizo mwako.
Umadziwa zoti kunjaku kulimatenda.
Ndipati sufuna kukonda wina.
Olo akwanu amati zayine uyiwale.
Ndipamene umandikondabe.
Nanenso ndidzakukonda.
Koma vuto ndiakwanu aja.
Ndizoti sandifuna.
Sindikudziwa kuti ndidzatani.
Ndiwe amene ungandilimbitse mtimaa.
(Corus)
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
Dziwa zoti akwanu sandifunaa.
Aaa eee ooo.
iwe ndi ine timakondana.
Sindikudziwa kuti ndidzapange chani.
Kuti tisazasiyaneee ooo.
ALEX BITON ON THE BEATS